Pa mtundu wa Ansenga
The Nsenga people are believed to have migrated into Zambia around the 14th century from the Luba-Lunda kingdom as a distinct language. Nsenga means "land of sand". The Nsenga people share much more same culture with the Lala people. The strong historical assumption is that the Nsenga people followed the same pattern of movements as the Lamba, Swaka, Lala and Bisa.
Ntchito ya Kutapulusa Baibolo mu Chisenga
Ntchito ya kutapulusa Baibolo mu chinsenga yeyamba mu Mwezi wa March 2010 ku Petauke, pa msonkhano wa magulu ngati Nsenga Bible Translation Project (NBTP) na Bible Society of Zambia (BSZ). Pambuyo pake, atsogoleri a mipingo, akulu a komiti, mafumu, na akulu a boma analowa nawo ntchito iyi. Mu May 2010, Bible Society of Zambia anakumana na nthumwi za Lutheran Bible Translators (LBT).
ŵelengani Bayibo mu Cinsenga
Mvwani Bayibo mu Cinsenga
Onani Yesu Filimu